Michael Servetus, William Tyndale ndi anthu enanso anaika moyo wawo pangozi chifukwa choti ankakonda kwambiri choonadi cha m’Baibulo.