Pitani ku nkhani yake

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Dzina la Mulungu Limapezekanso mu Mpukutu Wakale

Akatswiri akusonyeza kuti mpukutu wakale womwe unali ndi dzina la Yehova ndi umene unathandiza omasulira Baibulo kuti abwezeretse dzinali m’malo ake oyenera m’Malemba Achigiriki.