Pitani ku nkhani yake

Kuwerenga Komanso Kuphunzira Baibulo

Kuwerenga Baibulo

Kodi Ubwino Wowerenga Baibulo Ndi Wotani?

Kodi anthu ambiri apindula bwanji ndi kuwerenga Baibulo?

Njira Zowerengera Baibulo

Ndandandayi ingakuthandizeni kwambiri kaya mukufuna kumangowerenga Baibulo tsiku lililonse, kukhala ndi cholinga chomaliza kuwerenga Baibulo chaka chimodzi kapena kutsatira ndondomeko yowerengera Baibulo ya anthu omwe angoyamba kumene.

Kodi Baibulo Lingandithandize Bwanji?—Gawo 1: Kuganizira Mozama Mfundo za M’baibulo

Tiyerekeze kuti mwaona chikwama cha ndalama chomwe chikuoneka kuti ndi chakalekale, kodi simungakhale ndi chidwi kuti muone zimene zili mkatimo? Baibulo lili ngati chikwama choterocho. Mumapezeka mfundo zambiri zothandiza.

Kodi Baibulo Lingandithandize Bwanji?—Gawo 2: Zimene Mungachite Kuti Kuwerenga Baibulo Kuzikusangalatsani

Zinthu 5 zomwe zingakuthandizeni kuti muziona zimene mukuwerenga m’Baibulo kuti ndi zenizeni.

Kuphunzira Baibulo

N’chifukwa Chiyani Muyenera Kuphunzira Baibulo?

Kodi mumaona kuti simungapeze nthawi yophunzira Baibulo komanso kuti kuphunzira Baibulo n’kovuta? Kapena mumaopa kupangana ndi wa Mboni kuti azikuphunzitsani Baibulo chifukwa choona kuti zimenezi n’zopanikiza?

Baibulo Ndi Buku Lothandiza Kwambiri

Anthu ambiri amaona kuti Baibulo ndi buku lofunika, koma sadziwa kuti lingawathandize kwambiri pa moyo wawo.

N’chiyani Chingakuthandizeni Kumvetsa Baibulo?

Kaya ndife anthu otani, tikhoza kumvetsa uthenga wa Mulungu umene uli m’Malemba Opatulika.