Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

Malangizo Othandiza kwa Anthu Apabanja Ndiponso Makolo

“Kodi n’zotheka kukhala osangalala m’chaka chathu choyamba cha ukwati?” “Nthawi zonse tikamakambirana, timangokangana. Kaya tingatani kuti zimenezi zisamachitike?” “Kodi ndingatani kuti ndizikambirana ndi ana anga nkhani zokhudza kugonana?” Awa ndi ena mwa mafunso ambirimbiri amene anthu omwe ali pabanja angakhale nawo. Komanso pali malangizo osiyanasiyana amene amaperekedwa pa nkhani imeneyi.

Zilibe kanthu kuti ndinu wamtundu kapena chikhalidwe chotani, koma malangizo amene ali m’Baibulo angakuthandizeni kuti mukhale ndi banja losangalala komanso kuti mulere bwino ana anu.

Mabanja

Makolo