Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZITHUNZI

ZITHUNZI

Kodi Ndi Ndani Amene Anasankha Kutumikira Yehova?

Sankhani anthu otchulidwa m’Baibulo ndiponso mawu amene akufotokoza zimene anthuwo anachita. Sankhaninso anthu amene ankatumikira Mulungu.

Davide Analimba Mtima Ngakhale Kuti Anali ndi Zida Zochepa

Fananitsani anthu otchulidwa m’Baibulo ndi zinthu zokhudza anthuwo.

Davide Anabwera M’dzina la Mulungu

Thandizani ana anu kuti adziwe zimene dzina la Mulungu limatanthauza.

Hana Anathandiza Samueli Kuti Atumikire Yehova

Zochitazi zingathandize ana a pakati pa zaka zitatu ndi 6 kuti adziwe za mphatso imene Hana ankapatsa Samueli chaka chilichonse.