Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZITHUNZI ZOFOTOKOZA NKHANI ZA M’BAIBULO

ZITHUNZI ZOFOTOKOZA NKHANI ZA M’BAIBULO

Adamu ndi Hava Anachita Zinthu Modzikonda

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe za Adamu ndi Hava omwe anasankha zinthu modzikonda ndipo zinachititsa kuti anthu onse azikumana ndi mavuto. Werengani nkhaniyi pawebusaiti yathu kapena patsamba limene mwasindikiza.

Nowa Ankakhulupirira Kwambiri Mulungu

Nowa anamvera Mulungu ndipo anamanga chingalawa kuti apulumutse banja lake ku chigumula. Kodi nkhani ya Nowa ndi chigumula ikukuphunzitsani chiyani zokhudza kukhulupirira Mulungu?

Abulahamu Anali Bwenzi la Mulungu

Mulungu ananena kuti Abulahamu anali bwenzi lake. Kodi ifeyo tingatani kuti tikhale mabwenzi a Mulungu?

Rahabi Anatsatira Malangizo

Banja limodzi linapulumuka nthawi imene mzinda wa Yeriko unagwa.