Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Manowa

Pangani dawunilodi khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zokhudza Manowa, yemwe anali bambo wake wa munthu wamphamvu kwambiri. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.

Onani Zonse

Zinanso

Mfumu Sauli

Sauli atangoyamba kulamulira monga mfumu yoyamba ya Isiraeli, anali wodzichepetsa.

Hana

Mulungu anayankha pemphero lake.

Naomi

Mwamuna wake ndi ana ake aamuna atamwalira anapempha anzake kuti azimutchula dzina lina.