Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Hana

Pangani dawunilodi khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zokhudza Hana, yemwe anali mayi ake a mneneri Samueli. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.

Mfumu Sauli

Sauli atangoyamba kulamulira monga mfumu yoyamba ya Isiraeli, anali wodzichepetsa.

Manowa

Anali bambo wa munthu wamphamvu kwambiri.

Naomi

Mwamuna wake ndi ana ake aamuna atamwalira anapempha anzake kuti azimutchula dzina lina.