Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ACHINYAMATA ACHITE

ZOTI MUCHITE

Kulimbana ndi Vuto Losowa Ocheza Nawo

Tsamba limene mungalembepo zina n’zina zokuthandizani kuti mupeze anthu ocheza nawo kapena muyambenso kucheza ndi anthu amene munkacheza nawo m’mbuyomu.

Onani Zonse

Zinanso

Kodi Mungafotokoze Bwanji Zimene Mumakhulupirira pa Nkhani ya Kugonana kwa Amuna Kapena Akazi Okhaokha?

Kukambirana nkhani ngati izi kumakhala kovuta. Tsambali lingakuthandizeni kuti muzifotokoza mwanzeru komanso mosamala maganizo anu pa nkhani ya kugonana kwa amuna kapena akazi okhaokha.

Ngati Bambo Kapena Mayi Anu Akudwala

Mfundo za patsambali zingakuthandizeni posamalira bambo kapena mayi anu amene akudwala matenda aakulu komanso podzisamalira nokha.

Musamapitirire Malire

Muzitumiza mameseji oyenera kwa anzanu amene si amuna kapena akazi anu.