Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

Zimene Achinyamata Anzanu Amanena

Maonekedwe

Maonekedwe

Mu vidiyoyi achinyamata akufotokoza mavuto amene amakumana nawo kuti azisangalala ndi mmene amaonekera.

 

Onaninso

Kodi Ndimangokhalira Kuganizira za Maonekedwe Anga?

Kodi mungatani kuti muzisangalala ndi mmene mumaonekera?

Kodi Ndimakonda Kuvala Zovala Zotani?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zokhudza maganizo olakwika amene anthu amakhala nawo pa nkhani ya mafasho.

N’chifukwa Chiyani Sindikuyenera Kutsanzira Khalidwe la Anthu Omwe Amaonetsedwa M’mafilimu, pa TV ndi M’magazini?—Gawo 1: Ya Atsikana

Achinyamata ambiri amaganiza kuti akuchita zinthu m’njira yawoyawo, koma amakhala akungotsanzira zochita za ena.

N’chifukwa Chiyani Sindikuyenera Kutsanzira Khalidwe la Anthu Omwe Amaonetsedwa M’mafilimu, pa TV ndi M’magazini?—Gawo 2: Ya Anyamata

Kodi kutsanzira makhalidwe a anthu amene amasonyezedwa m’mafilimu, pa TV ndi m’magazini kungapangitse kuti anthu asamakopeke nanu?