Zokhudza screen reader

Sankhani chinenero

Pitani ku menyu yachiwiri

Pitani ku nkhani yake

Mboni za Yehova

Chichewa

MAVIDIYO AMAKATUNI

Musamangotengera Zochita za Anzanu

Musamangotengera Zochita za Anzanu

Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zingakuthandizeni kuti musamatengere zochita za anzanu.

Onaninso

Kodi Mungatani Kuti Musamangotengera Zochita za Anzanu?

Munthu akhoza kuyamba kuchita zoipa chifukwa chotengera zochita za anzake. Zimene muyenera kudziwa zokhudza kutengera zochita za anzanu komanso zimene mungachite pothetsa vutoli.

Kodi Anzanu Akukukakamizani Kuti Muzichita Zoipa?

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe mfundo zimene zingakuthandizeni kupewa, kapena kuthana ndi mayesero okhudza anzanu amene angakukakamizeni kuchita zoipa.

Kodi Akukukakamizani Kuti Mugone Naye?

Kodi ndibwino kungololera wina akamakukakamizani kuti mugonane? Kodi simudzanong’oneza bondo?