Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA

ZOTI MUCHITE POPHUNZIRA

Mzimu Woyera Umatulutsa Makhalidwe Abwino

Onani makhalidwe 9 omwe mzimu woyera wa Mulungu umatulutsa.

Imbani Nyimbo Yothandiza Kukhala Olimba Mtima

Phunzirani nyimbo imene imatithandiza kukhala olimba mtima ndipo kenako muimbe limodzi ndi banja lanu.

Kodi Mungalimbikitse Ndani?

Zochitazi zingathandize ana a pakati pa zaka 8 ndi 12 kuti adziwe zimene angachite kuti alimbikitse munthu.

Makhalidwe Omwe Munthu Wabwino Ayenera Kukhala Nawo

Zithunzizi n’zothandiza ana a zaka 8 mpaka 12 kuti akhale ndi makhalidwe abwino.