Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA

ZOTI MUCHITE POPHUNZIRA

Kodi Mungalimbikitse Ndani?

Limbikitsani munthu wina kuti azitumikira Yehova ngati mmene Elikana ndi Hana anachitira ndi Samueli.

Imbani Nyimbo Yothandiza Kukhala Olimba Mtima

Phunzirani nyimbo imene imatithandiza kukhala olimba mtima ndipo kenako muimbe limodzi ndi banja lanu.

Mzimu Woyera Umatulutsa Makhalidwe Abwino

Zochitazi zingathandize ana azaka za pakati pa 8 ndi 12 kuti aphunzire makhalidwe amene mzimu woyera umatulutsa.

Makhalidwe Omwe Munthu Wabwino Ayenera Kukhala Nawo

Zithunzizi n’zothandiza ana a zaka 8 mpaka 12 kuti akhale ndi makhalidwe abwino.