Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI ANA ACHITE POPHUNZIRA

Zoti Muchite Pophunzira

Mibadwo ya Banja la Loti

Koperani nkhaniyi, kuti muphunzire zokhudza mibadwo ya banja la Loti, yemwe anali m’bale wake wa Abulahamu.

Imbani Nyimbo Yothandiza Kukhala Olimba Mtima

Phunzirani nyimbo imene imatithandiza kukhala olimba mtima ndipo kenako muimbe limodzi ndi banja lanu.

Kodi Mungalimbikitse Ndani?

Zochitazi zingathandize ana a pakati pa zaka 8 ndi 12 kuti adziwe zimene angachite kuti alimbikitse munthu.

Mzimu Woyera Umatulutsa Makhalidwe Abwino

Zochitazi zingathandize ana azaka za pakati pa 8 ndi 12 kuti aphunzire makhalidwe amene mzimu woyera umatulutsa.