Pitani ku nkhani yake

ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA

Yehova Amatipatsa Mphamvu

OWERUZA CHAPUTALA 6 NDI 7

Zothandiza Makolo: Gwiritsani ntchito zochitazi pophunzira Baibulo monga banja.

ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA

Yehova Amatipatsa Mphamvu

OWERUZA CHAPUTALA 6 NDI 7

Zothandiza Makolo: Gwiritsani ntchito zochitazi pophunzira Baibulo monga banja.

Kuchita Zinthu Molimba Mtima

Phunzitsani ana anu zinthu zimene zimathandiza munthu kuti akhale wolimba mtima.

Kusankha Kutumikira Yehova

Tsambali lingakuthandizeni kuti muphunzitse ana anu zimene angachite kuti azitumikira Yehova mosangalala.

Mmene Mzimu Woyera Umatithandizira Kuti Tizitumikira Yehova

Gwiritsani ntchito tsambali pothandiza ana anu kuti aphunzire mmene Yehova amatithandizira ndi mzimu wake.