Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA

ZOCHITA PA KULAMBIRA KWA PABANJA

Mmene Mzimu Woyera Umatithandizira Kuti Tizitumikira Yehova

OWERUZA 13 MPAKA 16

Zothandiza Makolo: Gwiritsani ntchito zochitazi pophunzira Baibulo monga banja.

Kuchita Zinthu Molimba Mtima

Phunzitsani ana anu zinthu zimene zimathandiza munthu kuti akhale wolimba mtima.

Kusankha Kutumikira Yehova

Tsambali lingakuthandizeni kuti muphunzitse ana anu zimene angachite kuti azitumikira Yehova mosangalala.

Kukhala Ogwirizana Kwambiri

Malangizowa angakuthandizeni kuphunzitsa ana anu nkhani ya m’Baibulo ya Rute yosonyeza makhalidwe abwino amene anawo ayenera kukhala nawo.