Koperani ndi kusindikiza chithunzichi. Ndiyeno malizitsani kujambula chithunzichi kenako muyankhe mafunso amene ali pachithunzicho pamodzi ndi banja lanu.