Werengani za Yosefe. Iye anakhala kapolo ku Iguputo koma sanasiye kulambira Mulungu. Werengani nkhaniyi pawebusaitiyi kapena patsamba limene mwasindikiza.