Pitani ku nkhani yake

ZITHUNZI ZOFOTOKOZA NKHANI ZA M’BAIBULO

Yehova Anathandiza Solomo Kuti Akhale Wanzeru

Mu nkhani ya m’Baibuloyi, muona mmene Solomo anakhalira wanzeru koma kenako anapanga machimo akuluakulu. Werengani nkhaniyi pa intaneti kapena sindikizani PDF.