Pitani ku nkhani yake

ZITHUNZI ZOFOTOKOZA NKHANI ZA M’BAIBULO

Rahabi Anatsatira Malangizo

Kodi Rahabi anatani kuti apulumuke pamene Aisiraeli ankafuna kuwononga mzinda wa Yeriko? Mukhoza kuwerenga nkhaniyi pawebusaitiyi kapena patsamba limene mwasindikiza.