Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene Yehova Mulungu anachita posonyeza kuti ndi wamphamvu kuposa Farao wa ku Iguputo amene anali wouma mtima. Mukhoza kuwerenga nkhaniyi pawebusaitiyi kapena patsamba limene mwasindikiza.