Ngakhale kuti Davide anali mnyamata, anadalira kwambiri Yehova ndipo analimba mtima n’kugonjetsa Goliyati yemwe anali wamphamvu kwambiri. Werengani nkhaniyi pawebusaiti yathu kapena sindikizani tsambali.