Werengani nkhani yofotokoza za Aroni mchimwene wake wa Mose, pamene anachimwa chifukwa chothandiza Aisiraeli kupanga fano la mwana wa ng’ombe wagolide. Werengani nkhaniyi pa Intaneti kapena patsamba limene mwasindikiza.