Pitani ku nkhani yake

Zimene Ndikuphunzira M’Baibulo

Thokoza Mulungu Chifukwa cha Mvula

Nkhanizi ndi za ana osapitirira zaka zitatu. Koperani nkhaniyi kuti muwerengere mwana wanu.

Anyamata Atatu Achiheberi

Thandizani mwana wanu kudziwa chifukwa chimene chinachititsa Sadirake, Mesake ndi Abedinego kuti akane kugwadira fano la mfumu.

Yesu Ali Mwana

Phunzitsani mwana wanu wamng’ono zokhudza kubadwa kwa Yesu.

Madzi Anagawikana

Nkhani ya m’Baibulo ingakuthandizeni kuti muphunzitse mwana wanu nkhani yokhudza mmene Aisiraeli anawolokera Nyanja Yofiira.