Nkhani za m’Baibulo zino zalembedwa m’mawu osavuta kumva n’cholinga chothandiza makolo kuphunzitsa ana awo mfundo za m’Baibulo zomwe n’zothandiza. Nkhanizi zalembedwa m’njira yakuti makolo aziwerenga pamodzi ndi ana awo.