Yehova anapanga zinthu zokongola kuti anthufe tizisangalala chifukwa chakuti iye ndi Mnzathu. Kodi ungatchule zina mwa zinthu zomwe anapanga?