Pitani ku nkhani yake

Thandizani Kalebe Kukonza M’nyumba

Thandizani Kalebe Kukonza M’nyumba

Pangani dawunilodi tsambali, ndipo thandizani Kalebe kuti apeze zidole zake 5. Kalebe akufuna kumvera mayi ake pochotsa zidole zake m’nyumbamo.

 

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Uzikhala Waukhondo

Yehova amaika chilichonse pamalo oyenera. Onani zimene nanunso mungachite kuti muzikhala aukhondo