Pangani dawunilodi tsambali, ndipo muonere vidiyo yakuti “Tiyeni Tikalalikire.” Kenako lumikizani tizidutswa ta chikwama cha mu utumiki tomwe tili patsambali.