Tikakhala ndi zolinga zauzimu Yehova amaona kuti timaganizira kwambiri za iyeyo. Kodi iweyo uli ndi zolinga zotani?