Pitani ku nkhani yake

Muzipemphera Nthawi Iliyonse: Nyimbo ndi Mawu Ake

Muzipemphera Nthawi Iliyonse: Nyimbo ndi Mawu Ake

Pangani dawunilodi tsamba la nyimboli, ndipo muimbe limodzi ndi Sofiya. Mudziwanso nthawi komanso malo amene mungapemphere.

 

Onaninso

KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Muzipemphera Nthawi Iliyonse

Vidiyoyi ndi yoti mukhoza kuipanga dawunilodi ndipo imaphunzitsa ana nthawi komanso malo amene angapemphere kwa Yehova.