Pitani ku nkhani yake

Mmene Tingasonyezere Chikondi Kwa Ena

Mmene Tingasonyezere Chikondi Kwa Ena

Yesu anatisonyeza mmene tingasonyezere chikondi kwa anthu a m’banja lathu komanso anzathu. Tiyeni tione mmene tingachitire zimene.