Pitani ku nkhani yake

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—(Gawo 2)

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—(Gawo 2)

Tsatirani nyimboyi kuti muloweze mabuku ena 16 a Malemba Achiheberi.

Onaninso

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Lowezani Mabuku a M’Baibulo (Gawo 2)

Gwiritsani ntchito makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku a Malemba a Chiheberi, kuyambira Yeremiya mpaka Malaki.