Pitani ku nkhani yake

Phunziro 8: Uzikhala Waukhondo

Phunziro 8: Uzikhala Waukhondo

Kodi inuyo mukhoza kukhala aukhondo komanso oyera ngati Yehova? Kalebe anatengera chitsanzo cha Yehova pa nkhani imeneyi.

Mwina Mungakondenso Kudziwa Izi

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Thandizani Kalebe Kukonza M’nyumba

Pangani dawunilodi kapena sindikizani tsambali ndipo muthandizeni Kalebe kupeza zidole zake 5 zomwe akufunika kuchotsa m’nyumba.