N’chifukwa chiyani tiyenera kumvera makolo athu? Onerani vidiyoyi kuti mudziwe zimene zinathandiza Kalebe kuti aone chifukwa chake tiyenera kumvera makolo.