Pitani ku nkhani yake

Phunziro 16: Muzilalikira Anthu Olankhula Chinenero cha Dziko Lina

Phunziro 16: Muzilalikira Anthu Olankhula Chinenero cha Dziko Lina

Onani zimene zathandiza Kalebe ndi Sofiya kuti alalikire munthu wachinenero cha dziko lina.

Onaninso

ZOCHITA PA GAWO LA KHALANI BWENZI LA YEHOVA

Thandizani Anthu Ambiri Pogwiritsa Ntchito Pulogalamu Yothandiza Kuphunzira Chinenero pa JW

Phunzirani mawu a m’chinenero china kuti muzithandiza anthu kuphunzira zokhudza Yehova.