Kalebe ndi Sofiya akuphunzira kufunika kogawana zinthu ndi ena. Kodi nanunso mumagawana zinthu ndi ena?