Dzina la Yehova limasonyeza kuti iye ndi wodabwitsa kwambiri. Kodi iweyo ungauzeko ena za dzinali?