Pitani ku nkhani yake

Makadi a Anthu Otchulidwa M’Baibulo

Yonatani

Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti mudziwe za Yonatani. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.

Khadi la m’Baibulo Lonena za Mfumu Sauli

Sauli atangoyamba kulamulira monga mfumu yoyamba ya Isiraeli, anali wodzichepetsa.

Khadi la M’Baibulo la Hana

Mulungu anayankha pemphero lake.

Khadi la M’Baibulo la Manowa

Anali bambo wa munthu wamphamvu kwambiri.