Pangani dawunilodi khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zambiri za Rahabi, yemwe analimba mtima n’kubisa azondi awiri ochokera ku Isiraeli. Sindikizani, dulani, pindani pakati ndi kusunga.