MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Khadi la M’Baibulo Lonena za Miriamu

Chichewa
Khadi la M’Baibulo Lonena za Miriamu
https://cms-imgp.jw-cdn.org/img/p/502014101/univ/art/502014101_univ_sqr_xl.jpg

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Miriamu

Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti mudziwe za Miriamu, yemwe anali mchemwali wa Mose ndi Aroni. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.