Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Mfumu Sauli

Pangani dawunilodi khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zokhudza Sauli, yemwe poyamba anali wodzichepetsa koma kenako anayamba kudzikuza. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.

Khadi la M’Baibulo la Hana

Mulungu anayankha pemphero lake.

Khadi la M’Baibulo la Manowa

Anali bambo wa munthu wamphamvu kwambiri.

Khadi la M’Baibulo la Naomi

Mwamuna wake ndi ana ake aamuna atamwalira anapempha anzake kuti azimutchula dzina lina.