Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

MAKADI A ANTHU OTCHULIDWA M’BAIBULO

Gidiyoni

Pangani dawunilodi khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zokhudza Gidiyoni, munthu wodzichepetsa wa ku Isiraeli amene anakhala msilikali wolimba mtima. Sindikizani, dulani, pindani ndi kusunga.

Khadi la m’Baibulo Lonena za Mfumu Sauli

Sauli atangoyamba kulamulira monga mfumu yoyamba ya Isiraeli, anali wodzichepetsa.

Khadi la M’Baibulo la Hana

Mulungu anayankha pemphero lake.

Khadi la M’Baibulo la Manowa

Anali bambo wa munthu wamphamvu kwambiri.