Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti mudziwe za Danieli. Dulani, pindani ndi kusunga.