Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti muphunzire zambiri za Aroni, yemwe anali woyamba kukhala mkulu wa ansembe wa Aisiraeli. Sindikizani, dulani, pindani pakati ndi kusunga.