Koperani khadi la munthu wotchulidwa m’Baibuloli kuti mudziwe za Abele. Dulani, pindani ndi kusunga.