Dziwani nkhani za anthu osiyanasiyana amene amakuchititsani chidwi otchulidwa m’Baibulo. Koperani khadi lililonse, lisindikizeni, lipindeni pakati ndi kulisunga. Koperani ndi kusunga makadi onse.