Phunzirani zimene Baibulo limanena pa nkhani ya kupewa mizimu yoipa. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.