Pitani ku nkhani yake

Pitani ku menyu yachiwiri

Mboni za Yehova

Chichewa

ZOTI MUCHITE POPHUNZIRA BAIBULO

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Pirirani Mavuto Mosangalala

Phunzirani nkhani ya Paulo ndi Sila. Koperani nkhaniyi, iwerengeni m’Baibulo ndipo mukhale ngati mukuona zinthuzo zikuchitika.

Muzilandira Uphungu Modzichepetsa

Kodi mungaphunzirepo chiyani mukaganizira mmene Natani anaperekera uphungu kwa Davide?

Pewani Kulakalaka Zinthu Zoipa

Chitani zimene mwauzidwa kuti muchite, ndipo mukamawerenga nkhani ya m’Baibuloyi ya Davide ndi Bati-seba, muziyerekezera kuti mukuona zimene zikuchitikazo. Kodi tingaphunzirepo chiyani pa nkhaniyi?

Pewani Mtima Wodzikuza

Abisalomu, yemwe anali mwana wa Mfumu Davide, ankafuna kulanda ufumu wa bambo ake. Koma mtima wake wodzikuzawu unam’chititsa kuti ataye moyo wake.