Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Mose Anapatsidwa Utumiki Wapadera

Werengani nkhaniyi kuti mudziwe zimene tingachite kuti tikhale atumiki odalirika a Yehova ngakhale kuti ndife opanda ungwiro. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.