Pitani ku nkhani yake

Zoti Muchite Pophunzira Baibulo

Pewani Nsanje

Phunzirani nkhani ya Miriamu ndi Aroni. Koperani nkhani ya m’Baibuloyi, iwerengeni, ndipo muiganizire mozama n’kuona mmene ingakuthandizireni.

Muzilandira Uphungu Modzichepetsa

Kodi mungaphunzirepo chiyani mukaganizira mmene Natani anaperekera uphungu kwa Davide?

Pirirani Mavuto Mosangalala

Onani zimene zinathandiza Paulo ndi Sila kuti azisangalalabe ngakhale kuti ankazunzidwa.

Pewani Kulakalaka Zinthu Zoipa

Chitani zimene mwauzidwa kuti muchite, ndipo mukamawerenga nkhani ya m’Baibuloyi ya Davide ndi Bati-seba, muziyerekezera kuti mukuona zimene zikuchitikazo. Kodi tingaphunzirepo chiyani pa nkhaniyi?